Ezekieli 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho ndinanyamuka nʼkupita kuchigwako ndipo ndinaona kuti ulemerero wa Yehova uli kumeneko.+ Ulemerero umenewu unali wofanana ndi umene ndinauona pafupi ndi mtsinje wa Kebara+ ndipo ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi.
23 Choncho ndinanyamuka nʼkupita kuchigwako ndipo ndinaona kuti ulemerero wa Yehova uli kumeneko.+ Ulemerero umenewu unali wofanana ndi umene ndinauona pafupi ndi mtsinje wa Kebara+ ndipo ndinagwada nʼkuwerama mpaka nkhope yanga pansi.