Ezekieli 4:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndipo utenge tirigu, balere, nyemba zikuluzikulu, mphodza, mapira ndi sipeloti.* Zonsezo uziike mumphika umodzi kuti zikhale chakudya chako. Pa masiku 390 amene udzakhale ukugonera mbali imodzi uzidzadya chakudya chimenechi.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:9 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 12
9 Ndipo utenge tirigu, balere, nyemba zikuluzikulu, mphodza, mapira ndi sipeloti.* Zonsezo uziike mumphika umodzi kuti zikhale chakudya chako. Pa masiku 390 amene udzakhale ukugonera mbali imodzi uzidzadya chakudya chimenechi.+