-
Ezekieli 5:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Iwe mwana wa munthu, tenga lupanga lakuthwa kuti uligwiritse ntchito ngati lezala lometera. Umete tsitsi lako ndi ndevu zako ndipo kenako utenge sikelo nʼkuyeza tsitsilo. Ukatero uligawe mʼmagawo atatu.
-