Ezekieli 5:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anapandukira zigamulo zanga ndi malamulo anga pochita zoipa kuposa anthu amitundu inawo ndi mayiko amene amuzungulira.+ Anthu okhala mu Yerusalemu anakana zigamulo zanga ndipo sanatsatire malamulo anga.’
6 Iye anapandukira zigamulo zanga ndi malamulo anga pochita zoipa kuposa anthu amitundu inawo ndi mayiko amene amuzungulira.+ Anthu okhala mu Yerusalemu anakana zigamulo zanga ndipo sanatsatire malamulo anga.’