7 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Chifukwa chakuti anthu inu munali ovuta kuposa anthu a mitundu ina amene anakuzungulirani, ndipo simunatsatire malamulo anga, kapena kutsatira zigamulo zanga, koma munatsatira zigamulo za anthu a mitundu ina amene anakuzungulirani,+