Ezekieli 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho azibambo amene ali mumzindawo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumbali zonse.”’+
10 Choncho azibambo amene ali mumzindawo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumbali zonse.”’+