-
Ezekieli 5:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Udzakhala chinthu chimene anthu azidzachinyoza komanso kuchichitira chipongwe.+ Zimene zidzakuchitikire zidzakhala chenjezo ndipo zidzabweretsa mantha kwa anthu a mitundu yokuzungulira. Zimenezi zidzachitika ndikadzapereka chiweruzo kwa iwe komanso kukulanga mokwiya ndiponso mwaukali. Ineyo Yehova ndi amene ndanena zimenezi.
-