Ezekieli 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndidzakutumizira njala ndi zilombo zolusa+ ndipo zidzakuphera ana ako. Mliri komanso kuphana zidzakhala paliponse ndipo ndidzakubweretsera lupanga.+ Ineyo Yehova ndi amene ndanena zimenezi.’” Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:17 Nsanja ya Olonda,10/15/1988, tsa. 11
17 Ndidzakutumizira njala ndi zilombo zolusa+ ndipo zidzakuphera ana ako. Mliri komanso kuphana zidzakhala paliponse ndipo ndidzakubweretsera lupanga.+ Ineyo Yehova ndi amene ndanena zimenezi.’”