Ezekieli 6:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Maguwa anu ansembe adzagumulidwa, maguwa anu ofukizirapo zonunkhira adzaphwanyidwa+ ndipo mitembo ya anthu anu amene adzaphedwe ndidzaiponyera pamaso pa mafano anu onyansa.*+
4 Maguwa anu ansembe adzagumulidwa, maguwa anu ofukizirapo zonunkhira adzaphwanyidwa+ ndipo mitembo ya anthu anu amene adzaphedwe ndidzaiponyera pamaso pa mafano anu onyansa.*+