Ezekieli 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yemwe ali kutali adzaphedwa ndi mliri. Yemwe ali pafupi adzaphedwa ndi lupanga. Yemwe wapulumuka zinthu zimenezi adzafa ndi njala, ndipo ndidzawasonyeza mkwiyo wanga wonse.+
12 Yemwe ali kutali adzaphedwa ndi mliri. Yemwe ali pafupi adzaphedwa ndi lupanga. Yemwe wapulumuka zinthu zimenezi adzafa ndi njala, ndipo ndidzawasonyeza mkwiyo wanga wonse.+