-
Ezekieli 7:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 “Iwe mwana wa munthu, Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wauza dziko la Isiraeli kuti: ‘Mapeto afika! Mapeto afikira mbali zonse za dzikoli.
-