-
Ezekieli 7:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mapeto akufikira, ndipo ndisonyeza mkwiyo wanga wonse pa iwe. Ndidzakuweruza mogwirizana ndi njira zako ndiponso kukulanga chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene umachita.
-