Ezekieli 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Tsoka likubwera! Kukubwera tsoka loti silinaonekepo.+