Ezekieli 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Diso langa silidzakumvera chisoni ndipo sindidzakuchitira chifundo.+ Ndidzakulanga mogwirizana ndi njira zako moti udzakumana ndi mavuto chifukwa cha zinthu zonyansa zimene ukuchita. Udzadziwa kuti ine Yehova, ndi amene ndikukulanga.+
9 Diso langa silidzakumvera chisoni ndipo sindidzakuchitira chifundo.+ Ndidzakulanga mogwirizana ndi njira zako moti udzakumana ndi mavuto chifukwa cha zinthu zonyansa zimene ukuchita. Udzadziwa kuti ine Yehova, ndi amene ndikukulanga.+