Ezekieli 7:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chiwawa chasanduka ndodo yolangira zinthu zoipa.+ Kaya ndi anthuwo, chuma chawo, kuchuluka kwawo kapena kutchuka kwawo, palibe chimene chidzapulumuke.
11 Chiwawa chasanduka ndodo yolangira zinthu zoipa.+ Kaya ndi anthuwo, chuma chawo, kuchuluka kwawo kapena kutchuka kwawo, palibe chimene chidzapulumuke.