Ezekieli 7:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Nthawi idzakwana ndipo tsikulo lidzafika. Wogula asasangalale ndipo wogulitsa asalire, chifukwa mkwiyo wa Mulungu wayakira gulu lawo lonselo.*+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:12 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 13
12 Nthawi idzakwana ndipo tsikulo lidzafika. Wogula asasangalale ndipo wogulitsa asalire, chifukwa mkwiyo wa Mulungu wayakira gulu lawo lonselo.*+