Ezekieli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo avala ziguduli+ ndipo akungonjenjemera. Aliyense adzachititsidwa manyazi ndipo mitu yawo yonse idzakhala ndi mipala.*+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:18 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 13
18 Iwo avala ziguduli+ ndipo akungonjenjemera. Aliyense adzachititsidwa manyazi ndipo mitu yawo yonse idzakhala ndi mipala.*+