Ezekieli 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Iwo ankanyadira kukongola kwa zinthu zawo zodzikongoletsera. Ndipo pogwiritsa ntchito zinthu zimenezi* anapanga mafano awo onyansa.+ Nʼchifukwa chake ndidzachititse kuti zinthu zimenezi adzanyansidwe nazo.
20 Iwo ankanyadira kukongola kwa zinthu zawo zodzikongoletsera. Ndipo pogwiritsa ntchito zinthu zimenezi* anapanga mafano awo onyansa.+ Nʼchifukwa chake ndidzachititse kuti zinthu zimenezi adzanyansidwe nazo.