Ezekieli 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Panga unyolo+ chifukwa anthu osalakwa amene aweruzidwa mopanda chilungamo akuphedwa mʼdziko lonseli+ ndipo mumzinda mwadzaza chiwawa.+
23 Panga unyolo+ chifukwa anthu osalakwa amene aweruzidwa mopanda chilungamo akuphedwa mʼdziko lonseli+ ndipo mumzinda mwadzaza chiwawa.+