Ezekieli 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndidzabweretsa anthu oipa kwambiri a mitundu ina+ ndipo adzalanda nyumba zawo.+ Ndidzathetsa kunyada kwa anthu amphamvu ndipo malo awo opatulika adzaipitsidwa.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 7:24 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 13
24 Ndidzabweretsa anthu oipa kwambiri a mitundu ina+ ndipo adzalanda nyumba zawo.+ Ndidzathetsa kunyada kwa anthu amphamvu ndipo malo awo opatulika adzaipitsidwa.+