-
Ezekieli 8:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Mʼchaka cha 6, mʼmwezi wa 6, pa tsiku la 5 la mweziwo dzanja la Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, linandikhudza. Pa nthawiyo ndinali nditakhala mʼnyumba mwanga ndipo akuluakulu a Yuda anali atakhala pamaso panga.
-