Ezekieli 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho ndinalowa ndipo nditayangʼana ndinaona zithunzi za zinthu zosiyanasiyana zokwawa, nyama zonyansa+ komanso mafano onse onyansa* a Aisiraeli.+ Zithunzizo zinajambulidwa pamakoma onse mochita kugoba. Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 8:10 Nsanja ya Olonda,1/15/1993, tsa. 274/1/1986, ptsa. 19-20
10 Choncho ndinalowa ndipo nditayangʼana ndinaona zithunzi za zinthu zosiyanasiyana zokwawa, nyama zonyansa+ komanso mafano onse onyansa* a Aisiraeli.+ Zithunzizo zinajambulidwa pamakoma onse mochita kugoba.