-
Ezekieli 8:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Choncho anandipititsa pakhomo la geti la nyumba ya Yehova limene linali mbali yakumpoto ndipo kumeneko ndinaona azimayi atakhala pansi nʼkumalirira mulungu wotchedwa Tamuzi.
-