Ezekieli 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Iye anandiuzanso kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi ukuona zimenezi? Uonanso zinthu zina zoipa zomwe ndi zonyansa kwambiri kuposa zimenezi.”+
15 Iye anandiuzanso kuti: “Iwe mwana wa munthu, kodi ukuona zimenezi? Uonanso zinthu zina zoipa zomwe ndi zonyansa kwambiri kuposa zimenezi.”+