Ezekieli 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho ineyo ndidzawalanga nditakwiya kwambiri. Diso langa silidzawamvera chisoni ndipo sindidzawachitira chifundo.+ Ngakhale iwo adzandilirire mofuula, ine sindidzamva.”+
18 Choncho ineyo ndidzawalanga nditakwiya kwambiri. Diso langa silidzawamvera chisoni ndipo sindidzawachitira chifundo.+ Ngakhale iwo adzandilirire mofuula, ine sindidzamva.”+