-
Ezekieli 9:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Kenako iye analankhula mokuwa ine ndikumva, kuti: “Itana anthu amene akuyenera kupereka chilango pamzindawu. Aliyense abwere atanyamula chida chake chowonongera!”
-