Ezekieli 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anawauza kuti: “Ipitsani nyumbayi ndipo mudzaze mabwalo ake ndi mitembo ya anthu ophedwa.+ Pitani!” Choncho iwo anapitadi nʼkukapha anthu mumzindamo.
7 Kenako anawauza kuti: “Ipitsani nyumbayi ndipo mudzaze mabwalo ake ndi mitembo ya anthu ophedwa.+ Pitani!” Choncho iwo anapitadi nʼkukapha anthu mumzindamo.