Ezekieli 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno ulemerero wa Yehova+ unachoka pa akerubi nʼkupita pakhomo la nyumba yopatulika ndipo mtambo unayamba kudzaza nyumbayo pangʼonopangʼono.+ Komanso ulemerero wowala wa Yehova unadzaza mʼbwalo lonse la nyumbayo.
4 Ndiyeno ulemerero wa Yehova+ unachoka pa akerubi nʼkupita pakhomo la nyumba yopatulika ndipo mtambo unayamba kudzaza nyumbayo pangʼonopangʼono.+ Komanso ulemerero wowala wa Yehova unadzaza mʼbwalo lonse la nyumbayo.