Ezekieli 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pamene ndinkaona masomphenyawo, ndinaona kuti pambali pa akerubiwo panali mawilo 4. Pambali pa kerubi aliyense panali wilo limodzi ndipo mawilowo ankaoneka kuti akuwala ngati mwala wa kulusolito.+
9 Pamene ndinkaona masomphenyawo, ndinaona kuti pambali pa akerubiwo panali mawilo 4. Pambali pa kerubi aliyense panali wilo limodzi ndipo mawilowo ankaoneka kuti akuwala ngati mwala wa kulusolito.+