Ezekieli 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kerubi aliyense anali ndi nkhope 4. Nkhope yoyamba inali ya kerubi. Nkhope yachiwiri inali ya munthu. Nkhope yachitatu inali ya mkango ndipo nkhope ya 4 inali ya chiwombankhanga.+
14 Kerubi aliyense anali ndi nkhope 4. Nkhope yoyamba inali ya kerubi. Nkhope yachiwiri inali ya munthu. Nkhope yachitatu inali ya mkango ndipo nkhope ya 4 inali ya chiwombankhanga.+