Ezekieli 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 kapena akamayenda, mawilo aja ankayenda nawo limodzi ali pambali pawo. Akerubiwo akakweza mapiko awo kuti akwere mʼmwamba, mawilowo sankatembenuka kapena kuchoka pambali pawo.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, tsa. 15
16 kapena akamayenda, mawilo aja ankayenda nawo limodzi ali pambali pawo. Akerubiwo akakweza mapiko awo kuti akwere mʼmwamba, mawilowo sankatembenuka kapena kuchoka pambali pawo.+