-
Ezekieli 10:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Akerubiwo akaima, mawilonso ankaima. Akerubiwo akakwera mʼmwamba, mawilonso ankakwera nawo limodzi, chifukwa mzimu womwe unkatsogolera angelowo unkatsogoleranso mawilowo.
-