Ezekieli 10:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Angelo onse 4 anali ndi nkhope 4 komanso mapiko 4. Ndipo pansi pa mapiko awo panali chinachake chooneka ngati manja a munthu.+
21 Angelo onse 4 anali ndi nkhope 4 komanso mapiko 4. Ndipo pansi pa mapiko awo panali chinachake chooneka ngati manja a munthu.+