Ezekieli 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Inuyo mwachititsa kuti anthu ambiri afe mumzindawu ndipo mwadzaza misewu yake ndi anthu akufa.”’”+