Ezekieli 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mudzaphedwa ndi lupanga.+ Ndidzakuweruzirani mʼmalire a Isiraeli+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+
10 Mudzaphedwa ndi lupanga.+ Ndidzakuweruzirani mʼmalire a Isiraeli+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+