17 Choncho uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Kuwonjezera pamenepo ndidzakusonkhanitsani kuchokera kwa anthu a mitundu yosiyanasiyana ndiponso kuchokera mʼmayiko amene ndinakubalalitsiraniko ndipo ndidzakupatsani dziko la Isiraeli.+