Ezekieli 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo adzabwerera mʼdzikomo ndipo adzachotsamo mafano onse onyansa komanso adzasiya zinthu zonse zonyansa zimene amachita.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:18 Nsanja ya Olonda,5/1/1997, tsa. 20
18 Iwo adzabwerera mʼdzikomo ndipo adzachotsamo mafano onse onyansa komanso adzasiya zinthu zonse zonyansa zimene amachita.+