Ezekieli 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndiyeno akerubi aja anakweza mapiko awo mʼmwamba ndipo mawilo anali pambali pawo.+ Ulemerero wa Mulungu wa Isiraeli unali pamwamba pawo.+
22 Ndiyeno akerubi aja anakweza mapiko awo mʼmwamba ndipo mawilo anali pambali pawo.+ Ulemerero wa Mulungu wa Isiraeli unali pamwamba pawo.+