Ezekieli 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako ulemerero wa Yehova+ unakwera mʼmwamba kuchoka mumzindawo nʼkukaima pamwamba pa phiri, kumʼmawa kwa mzindawo.+ Ezekieli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:23 Nsanja ya Olonda,9/15/1988, ptsa. 16-17
23 Kenako ulemerero wa Yehova+ unakwera mʼmwamba kuchoka mumzindawo nʼkukaima pamwamba pa phiri, kumʼmawa kwa mzindawo.+