-
Ezekieli 11:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Ndiyeno mzimu unandinyamula nʼkukandisiya kudziko la Kasidi kumene kunali anthu ogwidwa ukapolo. Zimenezi zinachitika mʼmasomphenya amene ndinaona kudzera mwa mzimu wa Mulungu. Kenako masomphenya amene ndinaonawo anazimiririka.
-