-
Ezekieli 12:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Koma iweyo mwana wa munthu, longedza katundu wako woti upite naye ku ukapolo. Ndiyeno upite ku ukapolo masana anthuwo akuona. Uchoke kwanu kupita ku ukapolo kumalo ena, iwo akuona. Mwina azindikira tanthauzo lake ngakhale kuti iwo ndi anthu opanduka.
-