Ezekieli 12:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Iwe mwana wa munthu, idya chakudya chako ukunjenjemera ndipo umwe madzi uli ndi mantha ndiponso nkhawa.+
18 “Iwe mwana wa munthu, idya chakudya chako ukunjenjemera ndipo umwe madzi uli ndi mantha ndiponso nkhawa.+