Ezekieli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Iwe mwana wa munthu, kodi mwambi umene anthu amʼdziko la Isiraeli mukunena wakuti, ‘Masiku akupita koma palibe masomphenya amene akwaniritsidwa,’+ umatanthauza chiyani?
22 “Iwe mwana wa munthu, kodi mwambi umene anthu amʼdziko la Isiraeli mukunena wakuti, ‘Masiku akupita koma palibe masomphenya amene akwaniritsidwa,’+ umatanthauza chiyani?