Ezekieli 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Iwo aona masomphenya abodza ndipo alosera zonama. Akunena kuti, ‘Yehova wanena kuti,’ pamene Yehova sanawatume, ndipo akuyembekeza kuti zimene anenazo zichitika.+
6 “Iwo aona masomphenya abodza ndipo alosera zonama. Akunena kuti, ‘Yehova wanena kuti,’ pamene Yehova sanawatume, ndipo akuyembekeza kuti zimene anenazo zichitika.+