-
Ezekieli 13:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Choncho Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzatumiza mphepo yamkuntho yamphamvu komanso mvula yambiri posonyeza mkwiyo wanga. Ndidzatumiza matalala akuluakulu kuti awononge khomalo chifukwa ndakwiya kwambiri.
-