-
Ezekieli 13:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Uwauze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Tsoka akazi amene akusoka zinthu zovala mʼmikono* yonse ndi kupanga nsalu zophimba kumutu za mitu ya masaizi osiyanasiyana nʼcholinga choti akole anthuwo mumsampha nʼkuwapha. Kodi mukusaka miyoyo ya anthu anga nʼkumayesetsa kuti mupulumutse miyoyo yanu?
-