Ezekieli 14:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndidzadana naye munthuyo nʼkumuika kuti akhale chenjezo ndi mwambi ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu anga,+ moti mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’
8 Ine ndidzadana naye munthuyo nʼkumuika kuti akhale chenjezo ndi mwambi ndipo ndidzamupha kuti asakhalenso pakati pa anthu anga,+ moti mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’