Ezekieli 14:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “‘Kapenanso ngati nditatumiza mliri mʼdzikolo,+ nʼkulikhuthulira mkwiyo wanga pokhetsa magazi ambiri komanso kupha anthu ndi ziweto,
19 “‘Kapenanso ngati nditatumiza mliri mʼdzikolo,+ nʼkulikhuthulira mkwiyo wanga pokhetsa magazi ambiri komanso kupha anthu ndi ziweto,