-
Ezekieli 15:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ngakhale pamene mtengowo unali wathunthu sukanagwiritsidwa ntchito iliyonse. Ndiye kuli bwanji ukapsa ndi moto nʼkunyeka, kodi ungagwirenso ntchito iliyonse?”
-