Ezekieli 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Umuuze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, akuuza iwe Yerusalemu kuti: “Iwe unachokera kudziko la Akanani ndipo unabadwira komweko. Bambo ako anali a Chiamori+ ndipo mayi ako anali Muhiti.+
3 Umuuze kuti, ‘Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, akuuza iwe Yerusalemu kuti: “Iwe unachokera kudziko la Akanani ndipo unabadwira komweko. Bambo ako anali a Chiamori+ ndipo mayi ako anali Muhiti.+